Passar para o conteúdo principal

page search

Biblioteca Lamulo la Malo a Makolo 2016

Lamulo la Malo a Makolo 2016

Lamulo la Malo a Makolo 2016
Ndondomeko Yofotokozera Kalembera ndi Umwinimwini wa Malo a Makolo
Ndondomeko Yofotokozera Kalembera ndi Umwinimwini wa Malo a Makolo

Resource information

Date of publication
Fevereiro 2020
Resource Language
Pages
17

Msonkhano Wodziwitsa Atsogoleri a ma Dipatimenti ndi Mabungwe a pa Boma

Mamembala a nthambi yoyendetsa chitukuko pa Boma ayenera kudziwa za lamulo la malo a makolo koyambirira kuti asankhe dera lomwe angakayambire ntchito zokhudza lamuloli.

Msonkhano Wodziwitsa Makomiti a ADC, VDC ndi Magulu a m’madera za Lamulo la Malo a Makolo

Makomiti a ADC ndi VDC ndi ofunika kwambiri pothandiza anthu a m’madera mwawo kumvetsetsa za lamulo la malo a makolo.

Chisankho cha Komiti Yoyendetsa za Malo a Makolo

Anthu a m’midzi ya a Gulupu amasankha anthu omwe akuwafuna kuti akhale mamembala a komiti yoyendetsa za malo a makolo.

Maphunziro a Komiti Yowona za Malo a Makolo

Komiti yowona za malo a makolo iyenera kuphunzitsidwa za ntchito yake ndi akuluakulu a ku Unduna wa za Malo.

 

 

Share on RLBI navigator
NO